-
Ezekieli 33:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Kwa iwo uli ngati nyimbo yachikondi imene yaimbidwa mwaluso ndi choimbira cha zingwe komanso ndi mawu anthetemya. Iwo adzamva mawu ako, koma palibe amene adzawatsatire.
-