-
Ezekieli 34:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Kodi kudya msipu wabwino kwambiri si kokwanira kwa inu? Kodi mukuyeneranso kumapondaponda msipu wotsala ndi mapazi anu? Ndipo mukamaliza kumwa madzi oyera, kodi mukuyenera kuwadetsa powapondaponda ndi mapazi anu?
-