-
Ezekieli 34:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Kodi nkhosa zanga zizidya msipu umene inu mwaupondaponda ndi mapazi anu komanso kumwa madzi amene mwawadetsa powapondaponda ndi mapazi anu?”
-