-
Ezekieli 34:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Ndidzachita zimenezi chifukwa chakuti munkakankha nkhosa ndi nthiti zanu ndiponso mapewa anu. Ndipo munkagunda ndi nyanga zanu nkhosa zonse zodwala mpaka kuzibalalitsira kutali.
-