Ezekieli 34:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ine ndidzachita pangano lamtendere ndi nkhosazo.+ Ndipo ndidzachotsa zilombo zolusa mʼdzikomo+ nʼcholinga choti nkhosazo zizidzakhala mʼchipululu zili zotetezeka ndipo zizidzagona munkhalango.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:25 Galamukani!,4/8/1991, tsa. 11
25 Ine ndidzachita pangano lamtendere ndi nkhosazo.+ Ndipo ndidzachotsa zilombo zolusa mʼdzikomo+ nʼcholinga choti nkhosazo zizidzakhala mʼchipululu zili zotetezeka ndipo zizidzagona munkhalango.+