Ezekieli 34:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mitengo yamʼdzikomo idzabereka zipatso ndipo nthaka idzatulutsa zokolola zake.+ Iwo adzakhala mʼdzikolo motetezeka ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova ndikadzathyola goli lawo+ nʼkuwapulumutsa kwa anthu amene anawagwira kuti akhale akapolo awo. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:27 Nsanja ya Olonda,1/1/1993, tsa. 20
27 Mitengo yamʼdzikomo idzabereka zipatso ndipo nthaka idzatulutsa zokolola zake.+ Iwo adzakhala mʼdzikolo motetezeka ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova ndikadzathyola goli lawo+ nʼkuwapulumutsa kwa anthu amene anawagwira kuti akhale akapolo awo.