Ezekieli 34:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Anthu a mitundu ina sadzawagwiranso ndipo zilombo zolusa sizidzawadya. Iwo azidzakhala motetezeka popanda aliyense wowaopseza.+
28 Anthu a mitundu ina sadzawagwiranso ndipo zilombo zolusa sizidzawadya. Iwo azidzakhala motetezeka popanda aliyense wowaopseza.+