Ezekieli 35:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uuze deralo kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Iwe dera lamapiri la Seiri, ine ndikupatsa chilango. Nditambasula dzanja langa nʼkukukhaulitsa ndipo ndikusandutsa bwinja lowonongeka kwambiri.+
3 Uuze deralo kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Iwe dera lamapiri la Seiri, ine ndikupatsa chilango. Nditambasula dzanja langa nʼkukukhaulitsa ndipo ndikusandutsa bwinja lowonongeka kwambiri.+