Ezekieli 35:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mizinda yako ndidzaisandutsa bwinja komanso udzakhala malo owonongeka kwambiri+ ndipo udzadziwa kuti ine ndine Yehova.
4 Mizinda yako ndidzaisandutsa bwinja komanso udzakhala malo owonongeka kwambiri+ ndipo udzadziwa kuti ine ndine Yehova.