Ezekieli 35:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa chakuti unasonyeza chidani chachikulu+ ndipo unapha Aisiraeli ndi lupanga pa nthawi ya tsoka lawo, pamene ankalandira chilango chawo chomaliza.”’+
5 Chifukwa chakuti unasonyeza chidani chachikulu+ ndipo unapha Aisiraeli ndi lupanga pa nthawi ya tsoka lawo, pamene ankalandira chilango chawo chomaliza.”’+