Ezekieli 35:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ‘Choncho pali ine Mulungu wamoyo,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ‘Ndidzakonza zoti magazi ako akhetsedwe ndipo mlandu wa magazi udzakutsatira.+ Chifukwa unkadana ndi anthu amene unakhetsa magazi awo, mlandu wa magazi udzakutsatira.+
6 ‘Choncho pali ine Mulungu wamoyo,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ‘Ndidzakonza zoti magazi ako akhetsedwe ndipo mlandu wa magazi udzakutsatira.+ Chifukwa unkadana ndi anthu amene unakhetsa magazi awo, mlandu wa magazi udzakutsatira.+