-
Ezekieli 35:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Mʼmapiri amʼderalo ndidzadzazamo anthu amene aphedwa ndipo anthu amene aphedwa ndi lupanga adzagwera mʼzitunda zako, mʼzigwa zako ndi mʼmitsinje yako yonse.
-