Ezekieli 35:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 ‘Choncho pali ine Mulungu wamoyo,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ‘Ndidzakulanga mogwirizana ndi mkwiyo komanso nsanje imene unaisonyeza chifukwa chakuti unkadana nawo,+ ndipo ndikadzakuweruza, iwo adzandidziwa.
11 ‘Choncho pali ine Mulungu wamoyo,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, ‘Ndidzakulanga mogwirizana ndi mkwiyo komanso nsanje imene unaisonyeza chifukwa chakuti unkadana nawo,+ ndipo ndikadzakuweruza, iwo adzandidziwa.