Ezekieli 36:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Mdani wanu wakunenani kuti, ‘Eyaa! Ngakhale malo okwezeka akalekale tawatenga kuti akhale athu!’”’+
2 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Mdani wanu wakunenani kuti, ‘Eyaa! Ngakhale malo okwezeka akalekale tawatenga kuti akhale athu!’”’+