Ezekieli 36:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Ine ndikulumbira nditakweza dzanja langa kuti mitundu imene yakuzungulirani idzachita manyazi.+
7 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Ine ndikulumbira nditakweza dzanja langa kuti mitundu imene yakuzungulirani idzachita manyazi.+