Ezekieli 36:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndidzachulukitsa anthu anu. Ndidzachulukitsa nyumba yonse ya Isiraeli. Anthu adzayamba kukhala mʼmizinda+ ndipo malo amene anali mabwinja adzamangidwanso.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 36:10 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 24
10 Ndidzachulukitsa anthu anu. Ndidzachulukitsa nyumba yonse ya Isiraeli. Anthu adzayamba kukhala mʼmizinda+ ndipo malo amene anali mabwinja adzamangidwanso.+