11 Inde, ndidzachulukitsa anthu anu ndi ziweto zanu.+ Adzachuluka nʼkuberekana kwambiri. Ndidzachititsa kuti anthu akhale mwa inu ngati mmene zinalili poyamba+ ndipo ndidzachititsa kuti zinthu zikuyendereni bwino kwambiri kuposa poyamba.+ Choncho inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.+