Ezekieli 36:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndidzachititsa kuti anthu, anthu anga Aisiraeli, azidzayendayenda mwa inu ndipo adzakutengani kuti mukhale awo.+ Inu mudzakhala cholowa chawo ndipo simudzawalandanso ana awo.’”+
12 Ndidzachititsa kuti anthu, anthu anga Aisiraeli, azidzayendayenda mwa inu ndipo adzakutengani kuti mukhale awo.+ Inu mudzakhala cholowa chawo ndipo simudzawalandanso ana awo.’”+