-
Ezekieli 36:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Anthu akukunenani kuti: “Inu ndinu dziko limene limadya anthu ndipo mumapha ana a mitundu ya anthu anu.”’
-