Ezekieli 36:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 ‘Sindidzachititsanso kuti anthu a mitundu ina azikunyozani kapena kuti anthu azikunenerani mawu achipongwe+ ndipo simudzakhumudwitsanso mitundu ya anthu amene akukhala mwa inu,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
15 ‘Sindidzachititsanso kuti anthu a mitundu ina azikunyozani kapena kuti anthu azikunenerani mawu achipongwe+ ndipo simudzakhumudwitsanso mitundu ya anthu amene akukhala mwa inu,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”