Ezekieli 36:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Iwe mwana wa munthu, pa nthawi imene a nyumba ya Isiraeli ankakhala mʼdziko lawo, analidetsa ndi makhalidwe awo komanso zochita zawo.+ Kwa ine, khalidwe lawo linali ngati zonyansa za mkazi amene akusamba.+
17 “Iwe mwana wa munthu, pa nthawi imene a nyumba ya Isiraeli ankakhala mʼdziko lawo, analidetsa ndi makhalidwe awo komanso zochita zawo.+ Kwa ine, khalidwe lawo linali ngati zonyansa za mkazi amene akusamba.+