Ezekieli 36:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho ndinawakhuthulira mkwiyo wanga chifukwa cha magazi amene iwo anakhetsa mʼdzikoli+ komanso chifukwa chakuti anadetsa dzikoli ndi mafano awo onyansa.*+
18 Choncho ndinawakhuthulira mkwiyo wanga chifukwa cha magazi amene iwo anakhetsa mʼdzikoli+ komanso chifukwa chakuti anadetsa dzikoli ndi mafano awo onyansa.*+