Ezekieli 36:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiye ndinawabalalitsira kwa anthu a mitundu ina ndipo ndinawamwaza mʼmayiko osiyanasiyana.+ Ndinawaweruza mogwirizana ndi njira zawo komanso zochita zawo.
19 Ndiye ndinawabalalitsira kwa anthu a mitundu ina ndipo ndinawamwaza mʼmayiko osiyanasiyana.+ Ndinawaweruza mogwirizana ndi njira zawo komanso zochita zawo.