Ezekieli 36:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma atapita kwa anthu a mitundu inawo, anthuwo anadetsa dzina langa loyera+ ponena za iwowo kuti, ‘Awa ndi anthu a Yehova, koma anachoka mʼdziko lake.’ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 36:20 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 24
20 Koma atapita kwa anthu a mitundu inawo, anthuwo anadetsa dzina langa loyera+ ponena za iwowo kuti, ‘Awa ndi anthu a Yehova, koma anachoka mʼdziko lake.’