Ezekieli 36:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndidzachita zinthu zosonyeza kuti ndikudera nkhawa dzina langa loyera, limene nyumba ya Isiraeli yalidetsa pakati pa anthu a mitundu ina kumene iwo anapita.”+
21 Ndidzachita zinthu zosonyeza kuti ndikudera nkhawa dzina langa loyera, limene nyumba ya Isiraeli yalidetsa pakati pa anthu a mitundu ina kumene iwo anapita.”+