Ezekieli 36:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma dziwani izi: Ine sindikuchita zimenezi chifukwa cha inu,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. ‘Koma inu a nyumba ya Isiraeli, muchite manyazi ndipo muone kuti mwanyozeka chifukwa cha njira zanu.’
32 Koma dziwani izi: Ine sindikuchita zimenezi chifukwa cha inu,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. ‘Koma inu a nyumba ya Isiraeli, muchite manyazi ndipo muone kuti mwanyozeka chifukwa cha njira zanu.’