Ezekieli 36:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Pa tsiku limene ndidzakuyeretseni nʼkuchotsa zolakwa zanu zonse, ndidzachititsa kuti mʼmizinda yanu muzikhala anthu+ komanso kuti malo amene anali mabwinja amangidwenso.+
33 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Pa tsiku limene ndidzakuyeretseni nʼkuchotsa zolakwa zanu zonse, ndidzachititsa kuti mʼmizinda yanu muzikhala anthu+ komanso kuti malo amene anali mabwinja amangidwenso.+