Ezekieli 36:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Anthu a mitundu ina amene anatsala omwe akuzungulirani, adzadziwa kuti ine Yehova, ndamanga zinthu zimene zinagwetsedwa komanso kuti ndadzala mitengo mʼdziko limene linali bwinja. Ine Yehova ndanena zimenezi ndipo ndazichita.’+
36 Anthu a mitundu ina amene anatsala omwe akuzungulirani, adzadziwa kuti ine Yehova, ndamanga zinthu zimene zinagwetsedwa komanso kuti ndadzala mitengo mʼdziko limene linali bwinja. Ine Yehova ndanena zimenezi ndipo ndazichita.’+