-
Ezekieli 36:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Ine ndidzalolanso kuti a nyumba ya Isiraeli andipemphe kuti ndiwachulukitsire anthu awo ngati gulu la nkhosa ndipo ndidzachitadi zimenezo.
-