Ezekieli 36:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Mizinda imene inali mabwinja idzadzaza ndi anthu ochuluka+ ngati gulu la oyera ndiponso ngati nkhosa za ku Yerusalemu* pa nthawi ya zikondwerero,+ ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’”
38 Mizinda imene inali mabwinja idzadzaza ndi anthu ochuluka+ ngati gulu la oyera ndiponso ngati nkhosa za ku Yerusalemu* pa nthawi ya zikondwerero,+ ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’”