Ezekieli 37:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Mphamvu za Yehova zinayamba kugwira ntchito pa ine* moti mzimu wa Yehova unanditenga nʼkukandikhazika pakati pa chigwa+ ndipo mʼchigwamo munali mafupa okhaokha.
37 Mphamvu za Yehova zinayamba kugwira ntchito pa ine* moti mzimu wa Yehova unanditenga nʼkukandikhazika pakati pa chigwa+ ndipo mʼchigwamo munali mafupa okhaokha.