Ezekieli 37:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anandiyendetsa mʼchigwamo kuti ndione mafupa onsewo ndipo ndinaona kuti mʼchigwamo munali mafupa ambiri ndipo anali ouma kwambiri.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:2 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2016, tsa. 30
2 Iye anandiyendetsa mʼchigwamo kuti ndione mafupa onsewo ndipo ndinaona kuti mʼchigwamo munali mafupa ambiri ndipo anali ouma kwambiri.+