-
Ezekieli 37:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndidzakuikirani mitsempha komanso mnofu ndipo ndidzakukutirani ndi khungu nʼkuika mpweya mwa inu ndipo mudzakhala ndi moyo. Choncho mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’”
-