-
Ezekieli 37:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Choncho ine ndinalosera mogwirizana ndi zimene anandilamula. Nditangolosera, panamveka phokoso la mafupa kuti gobedegobede! Ndipo mafupawo anayamba kubwera pamodzi nʼkumalumikizana.
-