-
Ezekieli 37:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Kenako ndinaona mitsempha ndi mnofu zikukuta mafupawo ndipo khungu linabwera pamwamba pake. Koma mʼmafupawo munalibe mpweya.
-