Ezekieli 37:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho ndinalosera mogwirizana ndi zimene anandilamula ndipo mpweya* unalowa mwa iwo. Iwo anakhala ndi moyo ndipo anaimirira.+ Anali gulu lalikulu kwambiri la asilikali. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:10 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2016, ptsa. 30-31
10 Choncho ndinalosera mogwirizana ndi zimene anandilamula ndipo mpweya* unalowa mwa iwo. Iwo anakhala ndi moyo ndipo anaimirira.+ Anali gulu lalikulu kwambiri la asilikali.