Ezekieli 37:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Inu anthu anga, ine ndikadzatsegula manda anu nʼkukutulutsani mʼmandamo, mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”+
13 Inu anthu anga, ine ndikadzatsegula manda anu nʼkukutulutsani mʼmandamo, mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”+