Ezekieli 37:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiye uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine nditenga Aisiraeli kuchokera kwa anthu a mitundu ina kumene anapita. Ndidzawasonkhanitsa pamodzi kuchokera kumbali zonse ndipo ndidzawabweretsa mʼdziko lawo.+
21 Ndiye uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine nditenga Aisiraeli kuchokera kwa anthu a mitundu ina kumene anapita. Ndidzawasonkhanitsa pamodzi kuchokera kumbali zonse ndipo ndidzawabweretsa mʼdziko lawo.+