Ezekieli 37:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mtumiki wanga Davide adzakhala mfumu yawo+ ndipo onsewo adzakhala ndi mʼbusa mmodzi.+ Iwo adzayenda motsatira zigamulo zanga ndiponso kusunga malamulo anga mosamala kwambiri.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:24 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 25
24 Mtumiki wanga Davide adzakhala mfumu yawo+ ndipo onsewo adzakhala ndi mʼbusa mmodzi.+ Iwo adzayenda motsatira zigamulo zanga ndiponso kusunga malamulo anga mosamala kwambiri.+