Ezekieli 39:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzakubweza nʼkukutsogolera kuti uchoke kumadera akutali kwambiri akumpoto+ ndipo ndidzakubweretsa kumapiri a ku Isiraeli. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 39:2 Ulosi wa Danieli, tsa. 283
2 Ndidzakubweza nʼkukutsogolera kuti uchoke kumadera akutali kwambiri akumpoto+ ndipo ndidzakubweretsa kumapiri a ku Isiraeli.