Ezekieli 39:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ‘Ndidzatumiza moto kuti ukawononge Magogi komanso anthu amene akukhala motetezeka mʼzilumba,+ ndipo anthu adzadziwa kuti ine ndine Yehova.
6 ‘Ndidzatumiza moto kuti ukawononge Magogi komanso anthu amene akukhala motetezeka mʼzilumba,+ ndipo anthu adzadziwa kuti ine ndine Yehova.