-
Ezekieli 39:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 ‘Inde, zimene ulosiwu ukunena zidzachitika ndipo zidzakwaniritsidwa,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. ‘Tsiku limene ndakhala ndikunena lija ndi limeneli.
-