-
Ezekieli 39:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Iwo sadzafunika kunyamula mitengo kutchire kapena kutola nkhuni kunkhalango chifukwa chakuti adzagwiritsa ntchito zida zankhondozo pokoleza moto.’
‘Adzalanda zinthu za anthu amene anawalanda zinthu zawo ndipo adzatenga katundu wa anthu amene anatenga katundu wawo,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
-