-
Ezekieli 39:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 ‘Pa tsiku limenelo Gogi+ ndidzamupatsa malo kuti akhale manda ake ku Isiraeli komweko, mʼchigwa chimene anthu amene amapita kumʼmawa kwa nyanja amadutsa, ndipo chigwacho chidzatseka njira imene anthu amadutsa. Kumeneko nʼkumene adzaike mʼmanda Gogi limodzi ndi magulu onse a anthu amene ankamutsatira ndipo adzalitchula kuti Chigwa cha Hamoni-Gogi.*+
-