Ezekieli 39:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu onse amʼdzikolo adzagwira ntchito yoika mʼmanda anthuwo. Iwo adzatchuka chifukwa cha ntchito imeneyi pa tsiku limene ine ndidzalemekezeke,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
13 Anthu onse amʼdzikolo adzagwira ntchito yoika mʼmanda anthuwo. Iwo adzatchuka chifukwa cha ntchito imeneyi pa tsiku limene ine ndidzalemekezeke,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.