-
Ezekieli 39:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 ‘Anthu adzapatsidwa ntchito yoti azidzazungulira mʼdzikomo nthawi zonse nʼkumakwirira mitembo imene yatsala pamtunda kuti ayeretse dziko. Iwo adzakhala akufunafuna mitembo kwa miyezi 7.
-