Ezekieli 39:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthu amene akungodutsa mʼdzikolo akaona fupa la munthu, azidzaika chizindikiro pafupi ndi fupalo. Kenako anthu amene anapatsidwa ntchito yokwirira mitembo aja adzalikwirira mʼChigwa cha Hamoni-Gogi.+
15 Anthu amene akungodutsa mʼdzikolo akaona fupa la munthu, azidzaika chizindikiro pafupi ndi fupalo. Kenako anthu amene anapatsidwa ntchito yokwirira mitembo aja adzalikwirira mʼChigwa cha Hamoni-Gogi.+