Ezekieli 39:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 ‘Patebulo langa mudzadya nʼkukhuta nyama ya mahatchi, ya okwera magaleta, ya anthu amphamvu ndi asilikali osiyanasiyana,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
20 ‘Patebulo langa mudzadya nʼkukhuta nyama ya mahatchi, ya okwera magaleta, ya anthu amphamvu ndi asilikali osiyanasiyana,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.