Ezekieli 39:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 ‘Ndidzasonyeza ulemerero wanga pakati pa anthu a mitundu ina ndipo mitundu yonse ya anthu idzaona chiweruzo chimene ndapereka komanso mphamvu zimene* ndasonyeza pakati pawo.+
21 ‘Ndidzasonyeza ulemerero wanga pakati pa anthu a mitundu ina ndipo mitundu yonse ya anthu idzaona chiweruzo chimene ndapereka komanso mphamvu zimene* ndasonyeza pakati pawo.+