Ezekieli 39:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Akadzachititsidwa manyazi chifukwa cha zinthu zonse zosakhulupirika zimene anandichitira,+ adzakhala mʼdziko lawo motetezeka, popanda wowaopseza.+
26 Akadzachititsidwa manyazi chifukwa cha zinthu zonse zosakhulupirika zimene anandichitira,+ adzakhala mʼdziko lawo motetezeka, popanda wowaopseza.+